Yohane 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kufikira nthawi ino simunapemphepo chilichonse m’dzina langa. Pemphani ndipo mudzalandira, kuti chimwemwe chanu chisefukire.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:24 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 17 Nsanja ya Olonda,2/1/2008, ptsa. 11-14
24 Kufikira nthawi ino simunapemphepo chilichonse m’dzina langa. Pemphani ndipo mudzalandira, kuti chimwemwe chanu chisefukire.+