Yohane 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndalankhula zinthu izi kwa inu, kuti chimwemwe changa chikhale mwa inu, ndi kuti chimwemwe chanu chisefukire.+ 1 Yohane 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho tikulemba zimenezi kuti tikhale ndi chimwemwe chachikulu.+
11 “Ndalankhula zinthu izi kwa inu, kuti chimwemwe changa chikhale mwa inu, ndi kuti chimwemwe chanu chisefukire.+