Yohane 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndalankhula zinthu izi kwa inu, kuti chimwemwe changa chikhale mwa inu, ndi kuti chimwemwe chanu chisefukire.+ Yohane 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kufikira nthawi ino simunapemphepo chilichonse m’dzina langa. Pemphani ndipo mudzalandira, kuti chimwemwe chanu chisefukire.+
11 “Ndalankhula zinthu izi kwa inu, kuti chimwemwe changa chikhale mwa inu, ndi kuti chimwemwe chanu chisefukire.+
24 Kufikira nthawi ino simunapemphepo chilichonse m’dzina langa. Pemphani ndipo mudzalandira, kuti chimwemwe chanu chisefukire.+