Chivumbulutso 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Taona! Ndikubwera ngati mbala.+ Wodala ndi amene akhalabe maso+ ndi kukhalabe chivalire malaya ake akunja, kuti asayende wosavala anthu n’kuona maliseche ake.”+ Chivumbulutso 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Amene akuchitira umboni zinthu zimenezi akuti, ‘Inde, ndikubwera mofulumira.’”+ “Ame! Bwerani, Ambuye Yesu.”
15 “Taona! Ndikubwera ngati mbala.+ Wodala ndi amene akhalabe maso+ ndi kukhalabe chivalire malaya ake akunja, kuti asayende wosavala anthu n’kuona maliseche ake.”+
20 “Amene akuchitira umboni zinthu zimenezi akuti, ‘Inde, ndikubwera mofulumira.’”+ “Ame! Bwerani, Ambuye Yesu.”