Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 16
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 16:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 66:6; Chv 16:17
  • +Sl 69:24; Zef 3:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 220

Chivumbulutso 16:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:7
  • +Chv 20:11
  • +Eks 9:10; De 28:35
  • +Chv 13:16, 18
  • +Chv 13:15; 19:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 221-223

Chivumbulutso 16:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:8
  • +Chv 17:15
  • +Eks 7:20
  • +Yes 57:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 223-224

Chivumbulutso 16:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:10
  • +Sl 78:44
  • +Eks 7:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 224-225

Chivumbulutso 16:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 3:14; Chv 1:4
  • +Sl 145:17; Yer 3:12; Chv 15:4
  • +De 32:4; Sl 119:137

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Yandikirani, ptsa. 286-288

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 224-225

Chivumbulutso 16:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 9:5; Sl 79:3; Mt 23:35
  • +Yes 49:26
  • +Chv 18:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 30-31, 224-225

Chivumbulutso 16:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 6:3
  • +Sl 19:9; 119:137; Chv 19:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 224-225

Chivumbulutso 16:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:12
  • +Yes 49:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 225-227

Chivumbulutso 16:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 83:18
  • +Aro 13:1
  • +Chv 9:21; 14:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 225, 226-227

Chivumbulutso 16:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:1
  • +Eks 10:21; Yes 8:22; Aef 4:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 227-228

Chivumbulutso 16:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 228-229

Chivumbulutso 16:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 9:13
  • +Sl 137:1
  • +Yes 44:27; Yer 50:38
  • +Yes 44:28; Yer 51:57

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2022, tsa. 6

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2012, ptsa. 17-18

    9/15/1990, tsa. 29

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 229-230, 260-261

    Ulosi wa Danieli, tsa. 281

    Galamukani!,

    12/8/1989, ptsa. 23-26

Chivumbulutso 16:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 4:1
  • +Le 11:12
  • +Chv 12:3
  • +Chv 13:1
  • +Chv 13:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 230-231

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 18-19

Chivumbulutso 16:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ti 4:1
  • +Chv 13:13
  • +Sl 2:2
  • +Chv 18:3, 9
  • +Eze 38:16; Chv 19:19
  • +Yow 2:1
  • +Yes 13:6; Yer 25:33; Eze 30:3; Yow 1:15; 2:11; Zef 1:15; 2Pe 3:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2019, ptsa. 8-9

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/2015, tsa. 2

    9/1/2011, tsa. 10

    2/15/2009, tsa. 4

    4/1/2008, tsa. 31

    2/1/2007, tsa. 31

    12/1/2005, tsa. 4

    2/15/1986, tsa. 24

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 230-231, 285-286

    Kukambitsirana, ptsa. 37-42

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 18-20

Chivumbulutso 16:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 5:2; 2Pe 3:10
  • +Lu 21:36
  • +Chv 3:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 231-232

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2005, tsa. 18

    12/15/2003, tsa. 21

    12/1/1999, ptsa. 18-19

    3/1/1997, ptsa. 14-19

    5/1/1991, tsa. 21

Chivumbulutso 16:16

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “Aramagedo.” M’Chiheberi, mawuwa akutanthauza, “Phiri la Megido.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Mb 35:22; Zek 12:11; Chv 19:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2019, ptsa. 8-9

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2137

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/2012, ptsa. 5-6

    9/1/2011, tsa. 10

    4/1/2008, tsa. 31

    2/1/2007, tsa. 31

    12/1/2005, tsa. 4

    4/15/1997, tsa. 17

    5/15/1990, tsa. 6

    1/1/1989, ptsa. 16-17

    2/15/1986, tsa. 24

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 232-233, 285-286

    Galamukani!,

    7/8/2005, ptsa. 12-13

    Kukambitsirana, ptsa. 37-42

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 16-20

Chivumbulutso 16:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 2:2; 6:12
  • +Yes 66:6; Chv 16:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 233-234

Chivumbulutso 16:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 38:19
  • +Da 12:1
  • +Ahe 12:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 234

Chivumbulutso 16:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:18
  • +Chv 18:2
  • +Yer 25:15; Chv 15:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 234

Chivumbulutso 16:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 6:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 234

Chivumbulutso 16:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yob 38:22, 23; Yes 28:2
  • +Chv 16:9
  • +Eks 9:24; Chv 11:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2020, tsa. 15

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2019, tsa. 16

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2015, tsa. 16

    2/15/2009, tsa. 4

    7/15/2008, ptsa. 6-7

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2242

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 234

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 16:1Yes 66:6; Chv 16:17
Chiv. 16:1Sl 69:24; Zef 3:8
Chiv. 16:2Chv 8:7
Chiv. 16:2Chv 20:11
Chiv. 16:2Eks 9:10; De 28:35
Chiv. 16:2Chv 13:16, 18
Chiv. 16:2Chv 13:15; 19:20
Chiv. 16:3Chv 8:8
Chiv. 16:3Chv 17:15
Chiv. 16:3Eks 7:20
Chiv. 16:3Yes 57:20
Chiv. 16:4Chv 8:10
Chiv. 16:4Sl 78:44
Chiv. 16:4Eks 7:20
Chiv. 16:5Eks 3:14; Chv 1:4
Chiv. 16:5Sl 145:17; Yer 3:12; Chv 15:4
Chiv. 16:5De 32:4; Sl 119:137
Chiv. 16:6Ge 9:5; Sl 79:3; Mt 23:35
Chiv. 16:6Yes 49:26
Chiv. 16:6Chv 18:20
Chiv. 16:7Eks 6:3
Chiv. 16:7Sl 19:9; 119:137; Chv 19:2
Chiv. 16:8Chv 8:12
Chiv. 16:8Yes 49:10
Chiv. 16:9Sl 83:18
Chiv. 16:9Aro 13:1
Chiv. 16:9Chv 9:21; 14:7
Chiv. 16:10Chv 13:1
Chiv. 16:10Eks 10:21; Yes 8:22; Aef 4:18
Chiv. 16:11Chv 16:21
Chiv. 16:12Chv 9:13
Chiv. 16:12Sl 137:1
Chiv. 16:12Yes 44:27; Yer 50:38
Chiv. 16:12Yes 44:28; Yer 51:57
Chiv. 16:131Yo 4:1
Chiv. 16:13Le 11:12
Chiv. 16:13Chv 12:3
Chiv. 16:13Chv 13:1
Chiv. 16:13Chv 13:11
Chiv. 16:141Ti 4:1
Chiv. 16:14Chv 13:13
Chiv. 16:14Sl 2:2
Chiv. 16:14Chv 18:3, 9
Chiv. 16:14Eze 38:16; Chv 19:19
Chiv. 16:14Yow 2:1
Chiv. 16:14Yes 13:6; Yer 25:33; Eze 30:3; Yow 1:15; 2:11; Zef 1:15; 2Pe 3:12
Chiv. 16:151At 5:2; 2Pe 3:10
Chiv. 16:15Lu 21:36
Chiv. 16:15Chv 3:18
Chiv. 16:162Mb 35:22; Zek 12:11; Chv 19:19
Chiv. 16:17Aef 2:2; 6:12
Chiv. 16:17Yes 66:6; Chv 16:1
Chiv. 16:18Eze 38:19
Chiv. 16:18Da 12:1
Chiv. 16:18Ahe 12:26
Chiv. 16:19Chv 17:18
Chiv. 16:19Chv 18:2
Chiv. 16:19Yer 25:15; Chv 15:7
Chiv. 16:20Chv 6:14
Chiv. 16:21Yob 38:22, 23; Yes 28:2
Chiv. 16:21Chv 16:9
Chiv. 16:21Eks 9:24; Chv 11:19
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 16:1-21

Chivumbulutso

16 Kenako, ndinamva mawu ofuula+ ochokera m’malo opatulika akuuza angelo 7 aja kuti: “Pitani, kathireni mbale 7 za mkwiyo+ wa Mulunguzo kudziko lapansi.”

2 Mngelo woyamba+ anapita n’kukathira mbale yake padziko lapansi.+ Pamenepo mliri wa zilonda zopweteka ndi zonyeka+ unagwa pakati pa anthu amene anali ndi chizindikiro cha chilombo,+ amenenso anali kulambira chifaniziro chake.+

3 Mngelo wachiwiri+ anathira mbale yake m’nyanja.+ Ndipo nyanja inasanduka magazi+ ngati a munthu wakufa, moti chamoyo chilichonse m’nyanjamo chinafa.+

4 Mngelo wachitatu+ anathira mbale yake pamitsinje+ ndi pa akasupe amadzi, ndipo zonse zinasanduka magazi.+ 5 Ndiye ndinamva mngelo wokhala ndi ulamuliro pa madzi akunena kuti: “Inu Amene mulipo ndi amene munalipo,+ inu Wokhulupirika,+ ndinu wolungama chifukwa mwapereka zigamulo zimenezi,+ 6 pakuti iwo anakhetsa magazi a oyera ndi a aneneri.+ Ndipo inu mwawapatsa magazi+ kuti amwe, ndipo n’zowayenereradi.”+ 7 Kenako ndinamva guwa lansembe likunena kuti: “Inde, Yehova Mulungu, inu Wamphamvuyonse,+ zigamulo zanu n’zoona ndi zolungama.”+

8 Mngelo wachinayi+ anathira mbale yake padzuwa. Ndipo dzuwa linaloledwa kutentha+ anthu ndi moto. 9 Choncho anthu anapsa ndi kutentha kwakukulu. Koma iwo ananyoza dzina la Mulungu,+ amene ali ndi ulamuliro+ pa miliri imeneyi, ndipo sanalape kuti amupatse ulemerero.+

10 Mngelo wachisanu anathira mbale yake pampando wachifumu wa chilombo.+ Pamenepo ufumu wake unachita mdima,+ ndipo anthu anayamba kudziluma malilime chifukwa cha ululu. 11 Koma iwo ananyoza+ Mulungu wakumwamba chifukwa cha ululu wawo ndi zilonda zawo, ndipo sanalape ntchito zawo.

12 Mngelo wa 6+ anathira mbale yake pamtsinje waukulu wa Firate,+ ndipo madzi ake anauma,+ kuti njira ya mafumu+ ochokera kotulukira dzuwa ikonzedwe.

13 Kenako ndinaona mauthenga atatu onyansa ouziridwa,+ ooneka ngati achule,+ akutuluka m’kamwa mwa chinjoka,+ m’kamwa mwa chilombo,+ ndi m’kamwa mwa mneneri wonyenga.+ 14 Kwenikweni amenewa ndi mauthenga ouziridwa+ ndi ziwanda ndipo amachita zizindikiro.+ Mauthengawo akupita kwa mafumu+ a dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu, kuti awasonkhanitsire pamodzi kunkhondo+ ya tsiku lalikulu+ la Mulungu Wamphamvuyonse.+

15 “Taona! Ndikubwera ngati mbala.+ Wodala ndi amene akhalabe maso+ ndi kukhalabe chivalire malaya ake akunja, kuti asayende wosavala anthu n’kuona maliseche ake.”+

16 Ndipo anawasonkhanitsa pamodzi, kumalo amene m’Chiheberi amatchedwa Haramagedo.*+

17 Ndiyeno mngelo wa 7 anakhuthulira mbale yake pampweya.+ Atatero, kunamveka mawu ofuula+ kuchokera m’malo opatulika, kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Zachitika!” 18 Pamenepo kunachitika mphezi, kunamveka mawu, ndipo kunagunda mabingu. Kunachitanso chivomezi chachikulu+ chimene sichinachitikepo chikhalire anthu padziko lapansi,+ chivomezi+ champhamvu kwambiri, chachikulu zedi. 19 Pamenepo mzinda waukulu+ unagawika zigawo zitatu, ndipo mizinda ya mitundu ya anthu inagwa. Ndiyeno Mulungu anakumbukira Babulo Wamkulu,+ kuti amupatse kapu yokhala ndi vinyo wa mkwiyo wake waukulu.+ 20 Komanso, chilumba chilichonse chinathawa. Ngakhale mapiri sanapezeke.+ 21 Ndipo matalala aakulu,+ lililonse lolemera pafupifupi makilogalamu 20, anagwera anthu kuchokera kumwamba. Anthuwo ananyoza Mulungu+ chifukwa cha mliri wa matalalawo,+ pakuti mliriwo unali waukulu modabwitsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena