Chivumbulutso 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye wamwetsa mitundu yonse ya anthu+ vinyo wa mkwiyo, vinyo wa dama lake. Ndipo mafumu a dziko lapansi anachita naye dama.+ Amalonda oyendayenda+ a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zambiri zamtengo wapatali zimene mkazi ameneyu anadziunjikira mopanda manyazi.”+ Chivumbulutso 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Mafumu+ a dziko lapansi amene anachita naye dama ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye,+ poona utsi+ wofuka chifukwa cha kupsa kwake.
3 Iye wamwetsa mitundu yonse ya anthu+ vinyo wa mkwiyo, vinyo wa dama lake. Ndipo mafumu a dziko lapansi anachita naye dama.+ Amalonda oyendayenda+ a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zambiri zamtengo wapatali zimene mkazi ameneyu anadziunjikira mopanda manyazi.”+
9 “Mafumu+ a dziko lapansi amene anachita naye dama ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye,+ poona utsi+ wofuka chifukwa cha kupsa kwake.