Chivumbulutso 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno kunachita mphezi, kunamveka mawu, kunagunda mabingu komanso kunachita chivomerezi chachikulu chimene sichinachitikepo kuyambira pamene munthu analengedwa padziko lapansi.+ Chivomerezicho chinali champhamvu kwambiri komanso chachikulu. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:18 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 234
18 Ndiyeno kunachita mphezi, kunamveka mawu, kunagunda mabingu komanso kunachita chivomerezi chachikulu chimene sichinachitikepo kuyambira pamene munthu analengedwa padziko lapansi.+ Chivomerezicho chinali champhamvu kwambiri komanso chachikulu.