Chivumbulutso 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo kunachitika mphezi, kunamveka mawu, ndipo kunagunda mabingu. Kunachitanso chivomezi chachikulu+ chimene sichinachitikepo chikhalire anthu padziko lapansi,+ chivomezi+ champhamvu kwambiri, chachikulu zedi. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:18 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 234
18 Pamenepo kunachitika mphezi, kunamveka mawu, ndipo kunagunda mabingu. Kunachitanso chivomezi chachikulu+ chimene sichinachitikepo chikhalire anthu padziko lapansi,+ chivomezi+ champhamvu kwambiri, chachikulu zedi.