Chivumbulutso 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera mʼmalo opatulika+ akuuza angelo 7 aja kuti: “Pitani, kathireni mbale 7 za mkwiyo wa Mulunguzo padziko lapansi.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:1 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 220
16 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera mʼmalo opatulika+ akuuza angelo 7 aja kuti: “Pitani, kathireni mbale 7 za mkwiyo wa Mulunguzo padziko lapansi.”+