Chivumbulutso 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mngelo wa 7 anakhuthulira mbale yake pampweya. Atatero, kunamveka mawu ofuula kuchokera mʼmalo opatulika,+ kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Zachitika!”
17 Mngelo wa 7 anakhuthulira mbale yake pampweya. Atatero, kunamveka mawu ofuula kuchokera mʼmalo opatulika,+ kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Zachitika!”