Chivumbulutso 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera mʼmalo opatulika+ akuuza angelo 7 aja kuti: “Pitani, kathireni mbale 7 za mkwiyo wa Mulunguzo padziko lapansi.”+
16 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera mʼmalo opatulika+ akuuza angelo 7 aja kuti: “Pitani, kathireni mbale 7 za mkwiyo wa Mulunguzo padziko lapansi.”+