Chivumbulutso 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo matalala aakulu,+ lililonse lolemera pafupifupi makilogalamu 20, anagwera anthu kuchokera kumwamba. Anthuwo ananyoza Mulungu+ chifukwa cha mliri wa matalalawo,+ pakuti mliriwo unali waukulu modabwitsa.
21 Ndipo matalala aakulu,+ lililonse lolemera pafupifupi makilogalamu 20, anagwera anthu kuchokera kumwamba. Anthuwo ananyoza Mulungu+ chifukwa cha mliri wa matalalawo,+ pakuti mliriwo unali waukulu modabwitsa.