Ekisodo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho iwo anatenga mwaye wa mu uvuni ndi kuima pamaso pa Farao. Pamenepo Mose anauponya m’mwamba, ndipo unayambitsa zithupsa zomaphulika,+ pa anthu ndi nyama. Deuteronomo 28:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa zonyeka m’mawondo onse ndi m’ntchafu monse. Matenda amenewa adzayambira kumapazi mpaka paliwombo, ndipo sudzachira.+
10 Choncho iwo anatenga mwaye wa mu uvuni ndi kuima pamaso pa Farao. Pamenepo Mose anauponya m’mwamba, ndipo unayambitsa zithupsa zomaphulika,+ pa anthu ndi nyama.
35 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa zonyeka m’mawondo onse ndi m’ntchafu monse. Matenda amenewa adzayambira kumapazi mpaka paliwombo, ndipo sudzachira.+