Deuteronomo 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa za ku Iguputo,+ matenda a mudzi,* ziwengo ndi zotupa, ndipo sudzachira matenda amenewa. Yobu 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Satana anachoka pamaso pa Yehova+ n’kukagwetsera Yobu zilonda zopweteka,+ kuyambira kuphazi mpaka kumutu.
27 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa za ku Iguputo,+ matenda a mudzi,* ziwengo ndi zotupa, ndipo sudzachira matenda amenewa.
7 Kenako Satana anachoka pamaso pa Yehova+ n’kukagwetsera Yobu zilonda zopweteka,+ kuyambira kuphazi mpaka kumutu.