Ekisodo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo udzachuluka ndi kugwa ngati fumbi padziko lonse la Iguputo. Ukatero udzayambitsa zithupsa zimene zizidzaphulika+ pa anthu ndi nyama zomwe, m’dziko lonse la Iguputo.” Levitiko 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Ngati pakhungu la munthu pali chithupsa,+ ndipo kenako chapola, Yobu 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Khungu langa linakhala lakuda+ ndipo linayoyoka pathupi panga.Mafupa anga anatentha chifukwa chouma.
9 Pamenepo udzachuluka ndi kugwa ngati fumbi padziko lonse la Iguputo. Ukatero udzayambitsa zithupsa zimene zizidzaphulika+ pa anthu ndi nyama zomwe, m’dziko lonse la Iguputo.”
30 Khungu langa linakhala lakuda+ ndipo linayoyoka pathupi panga.Mafupa anga anatentha chifukwa chouma.