Levitiko 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Ngati pakhungu la munthu pali chithupsa,+ ndipo kenako chapola, Deuteronomo 28:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa zonyeka m’mawondo onse ndi m’ntchafu monse. Matenda amenewa adzayambira kumapazi mpaka paliwombo, ndipo sudzachira.+ Yobu 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Satana anachoka pamaso pa Yehova+ n’kukagwetsera Yobu zilonda zopweteka,+ kuyambira kuphazi mpaka kumutu.
35 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa zonyeka m’mawondo onse ndi m’ntchafu monse. Matenda amenewa adzayambira kumapazi mpaka paliwombo, ndipo sudzachira.+
7 Kenako Satana anachoka pamaso pa Yehova+ n’kukagwetsera Yobu zilonda zopweteka,+ kuyambira kuphazi mpaka kumutu.