Yobu 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mnofu wanga wakutidwa ndi mphutsi+ ndipo wamatirira fumbi,+Khungu langa lang’ambika n’kumatuluka mafinya.+ Salimo 119:83 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 83 Ndakhala ngati thumba lachikopa+ mu utsi,Koma sindinaiwale malangizo anu.+ Maliro 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano ayamba kuoneka akuda kuposa makala. Anthu sakuwazindikiranso mumsewu.+Khungu lawo lafota moti lamamatira kumafupa awo.+ Langoti gwaa ngati mtengo.
5 Mnofu wanga wakutidwa ndi mphutsi+ ndipo wamatirira fumbi,+Khungu langa lang’ambika n’kumatuluka mafinya.+
8 Tsopano ayamba kuoneka akuda kuposa makala. Anthu sakuwazindikiranso mumsewu.+Khungu lawo lafota moti lamamatira kumafupa awo.+ Langoti gwaa ngati mtengo.