Chivumbulutso 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mngelo wachiwiri anathira mbale yake mʼnyanja.+ Nyanjayo inasanduka magazi+ ngati a munthu wakufa, moti chamoyo chilichonse mʼnyanjamo chinafa.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:3 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 223-224
3 Mngelo wachiwiri anathira mbale yake mʼnyanja.+ Nyanjayo inasanduka magazi+ ngati a munthu wakufa, moti chamoyo chilichonse mʼnyanjamo chinafa.+