Chivumbulutso 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mngelo wa 7 anakhuthulira mbale yake pampweya. Atatero, kunamveka mawu ofuula kuchokera mʼmalo opatulika,+ kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Zachitika!” Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:17 Nsanja ya Olonda,2/15/2009, tsa. 4 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 233-234
17 Mngelo wa 7 anakhuthulira mbale yake pampweya. Atatero, kunamveka mawu ofuula kuchokera mʼmalo opatulika,+ kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Zachitika!”