Chivumbulutso 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Taonani! Ndikubwera mofulumira.+ Wosangalala ndi aliyense amene akutsatira mawu a ulosi amumpukutuwu.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:7 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 6, 314 Nsanja ya Olonda,12/1/1999, tsa. 19
7 Taonani! Ndikubwera mofulumira.+ Wosangalala ndi aliyense amene akutsatira mawu a ulosi amumpukutuwu.”+