2 Mtsinjewo unadutsa pakati pa msewu waukulu wamumzindawo. Kumbali zonse ziwiri za mtsinjewo kunali mitengo ya moyo imene inkabereka zipatso zokolola maulendo 12, ndipo inkabereka zipatso mwezi uliwonse. Masamba a mitengoyo anali ochiritsira mitundu ya anthu.+