Yobu 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kodi anakuvundukulira zipata za imfa,+Kapena zipata za mdima wandiweyani,+ kodi ungathe kuziona? Salimo 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikomereni mtima inu Yehova. Onani mmene anthu odana nane akundisautsira,+Inu Mulungu amene mukundinyamula kundichotsa pazipata za imfa.+
13 Ndikomereni mtima inu Yehova. Onani mmene anthu odana nane akundisautsira,+Inu Mulungu amene mukundinyamula kundichotsa pazipata za imfa.+