2 Samueli 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti mafunde akupha anandizungulira.+Panali chikhamu cha anthu opanda pake amene anali kundiopseza.+ Yobu 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kodi anakuvundukulira zipata za imfa,+Kapena zipata za mdima wandiweyani,+ kodi ungathe kuziona? Salimo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, mwanditulutsa m’Manda,+Mwandisunga ndi moyo, kuti ndisatsikire m’dzenje.+ Salimo 107:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Moyo wawo unaipidwa ndi chakudya cha mtundu uliwonse,+Ndipo anafika pazipata za imfa.+ Salimo 116:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zingwe za imfa zinandizungulira+Ndipo ndinasautsika ngati kuti ndili m’Manda.+Ndinapitiriza kusautsika ndi kukhala wachisoni,+ Yesaya 38:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndinati: “Pakatikati pa masiku anga ndidzalowa pazipata+ za Manda.Ndidzamanidwa zaka zanga zotsala.”+ Chivumbulutso 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+
5 Pakuti mafunde akupha anandizungulira.+Panali chikhamu cha anthu opanda pake amene anali kundiopseza.+
3 Zingwe za imfa zinandizungulira+Ndipo ndinasautsika ngati kuti ndili m’Manda.+Ndinapitiriza kusautsika ndi kukhala wachisoni,+
10 Ine ndinati: “Pakatikati pa masiku anga ndidzalowa pazipata+ za Manda.Ndidzamanidwa zaka zanga zotsala.”+
18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+