-
Salimo 9:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndikomereni mtima inu Yehova. Onani mmene anthu odana nane akundisautsira,+
Inu Mulungu amene mukundinyamula kundichotsa pazipata za imfa.+
-