Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 33:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iye amayandikira kudzenje,+

      Ndipo moyo wake umayandikira kwa akupha.

  • Yobu 38:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kodi anakuvundukulira zipata za imfa,+

      Kapena zipata za mdima wandiweyani,+ kodi ungathe kuziona?

  • Salimo 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndikomereni mtima inu Yehova. Onani mmene anthu odana nane akundisautsira,+

      Inu Mulungu amene mukundinyamula kundichotsa pazipata za imfa.+

  • Salimo 88:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pakuti ine ndakumana ndi masoka ochuluka,+

      Ndipo moyo wanga wayandikira ku Manda.+

  • Salimo 116:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Zingwe za imfa zinandizungulira+

      Ndipo ndinasautsika ngati kuti ndili m’Manda.+

      Ndinapitiriza kusautsika ndi kukhala wachisoni,+

  • Chivumbulutso 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena