Salimo 107:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Moyo wawo unaipidwa ndi chakudya cha mtundu uliwonse,+Ndipo anafika pazipata za imfa.+ Yesaya 38:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndinati: “Pakatikati pa masiku anga ndidzalowa pazipata+ za Manda.Ndidzamanidwa zaka zanga zotsala.”+
10 Ine ndinati: “Pakatikati pa masiku anga ndidzalowa pazipata+ za Manda.Ndidzamanidwa zaka zanga zotsala.”+