Salimo 69:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipulumutseni m’matope kuti ndisamire.+Ndipulumutseni kwa anthu odana nane+ ndiponso ku madzi akuya.+
14 Ndipulumutseni m’matope kuti ndisamire.+Ndipulumutseni kwa anthu odana nane+ ndiponso ku madzi akuya.+