Salimo 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Onani mmene adani anga achulukira,+Ndipo chifukwa cha chidani chawo chachikulu, amafuna kundichitira chiwawa.+ Salimo 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Musalole kuti anthu amene amadana ndi ine popanda chifukwa akondwere ndi kusautsika kwanga.+Ndipo musalole kuti anthu amene amandida popanda chifukwa anditsinzinire diso.+
19 Onani mmene adani anga achulukira,+Ndipo chifukwa cha chidani chawo chachikulu, amafuna kundichitira chiwawa.+
19 Musalole kuti anthu amene amadana ndi ine popanda chifukwa akondwere ndi kusautsika kwanga.+Ndipo musalole kuti anthu amene amandida popanda chifukwa anditsinzinire diso.+