Salimo 69:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndamila m’matope akuya, mmene mulibe malo oponda.+Ndalowa m’madzi akuya,Ndipo mtsinje wa madzi othamanga wandikokolola.+ Maliro 3:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu Yehova, ndaitana dzina lanu mofuula ndili m’dzenje lakuya kwambiri.+
2 Ndamila m’matope akuya, mmene mulibe malo oponda.+Ndalowa m’madzi akuya,Ndipo mtsinje wa madzi othamanga wandikokolola.+