Salimo 88:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwandiika m’dzenje lakuya kwambiri,M’malo a mdima, m’phompho lalikulu.+ Salimo 116:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma ndinaitana pa dzina la Yehova kuti:+“Inu Yehova, pulumutsani moyo wanga!”+ Salimo 130:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 130 Inu Yehova, pa nthawi imene zinthu zinandivuta kwambiri ndinaitana pa inu.+ Yona 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti:“Pamene ndinali m’masautso ndinaitana Yehova,+ ndipo anandiyankha.+Ndinafuula kupempha thandizo ndili m’Manda* akuya.+Ndipo inu munamva mawu anga.+
2 kuti:“Pamene ndinali m’masautso ndinaitana Yehova,+ ndipo anandiyankha.+Ndinafuula kupempha thandizo ndili m’Manda* akuya.+Ndipo inu munamva mawu anga.+