Salimo 130:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 130 Inu Yehova, pa nthawi imene zinthu zinandivuta kwambiri ndinaitana pa inu.+ Maliro 3:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu Yehova, ndaitana dzina lanu mofuula ndili m’dzenje lakuya kwambiri.+