Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 18:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Zingwe za Manda zinandizungulira.+

      Ndinayang’anizana ndi misampha ya imfa.+

  • Salimo 25:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Masautso a mtima wanga awonjezeka.+

      Ndilanditseni ku nkhawa zimene zili pa ine.+

  • Salimo 40:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Iye ananditulutsanso m’dzenje la madzi a mkokomo,+

      Ananditulutsa m’chithaphwi cha matope.+

      Kenako anapondetsa phazi langa pathanthwe.+

      Anandiyendetsa panthaka yolimba.+

  • Salimo 71:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Chifukwa chakuti mwandionetsa masautso ndi masoka ambiri,+

      Nditsitsimutseni.+

      Nditulutseninso m’madzi akuya, pansi pa nthaka.+

  • Maliro 3:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Inu Yehova, ndaitana dzina lanu mofuula ndili m’dzenje lakuya kwambiri.+

  • Yona 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 kuti:

      “Pamene ndinali m’masautso ndinaitana Yehova,+ ndipo anandiyankha.+

      Ndinafuula kupempha thandizo ndili m’Manda* akuya.+

      Ndipo inu munamva mawu anga.+

  • Aheberi 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamene anali munthu, Khristu anapereka mapemphero opembedzera ndi opempha,+ kwa amene anali wokhoza kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula+ komanso akugwetsa misozi, ndipo anamumvera chifukwa chakuti anali kuopa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena