2 Samueli 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zingwe za Manda* zinandizungulira.+Ndinakumana ndi misampha ya imfa.+ Salimo 88:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ine ndakumana ndi masoka ochuluka,+Ndipo moyo wanga wayandikira ku Manda.+