Salimo 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti iye sananyoze,+Kapena kunyansidwa ndi nsautso ya munthu wosautsidwa.+Ndipo sanam’bisire nkhope yake.+Pamene anamulirira kuti amuthandize, iye anamva.+ Salimo 120:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 120 Ndinafuulira Yehova m’masautso anga,+Ndipo iye anandiyankha.+
24 Pakuti iye sananyoze,+Kapena kunyansidwa ndi nsautso ya munthu wosautsidwa.+Ndipo sanam’bisire nkhope yake.+Pamene anamulirira kuti amuthandize, iye anamva.+