Salimo 69:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pakuti Yehova akumvetsera osauka,+Ndipo sadzanyoza anthu ake amene ali m’ndende.+