Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 10:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mudzamva kuchonderera kwa anthu ofatsa,+ inu Yehova.

      Mudzakonzekeretsa mitima yawo.+

      Mudzatchera khutu lanu,+

  • Salimo 102:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iye adzamvetsera pemphero la anthu amene alandidwa chilichonse,+

      Ndipo sadzapeputsa pemphero lawo.+

  • Yesaya 66:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Zinthu zonsezi ndinazipanga ndi dzanja langa, choncho zinakhalapo,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzayang’ana munthu amene ali wosautsidwa, wosweka mtima,+ ndiponso wonjenjemera ndi mawu anga.+

  • Luka 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Mzimu wa Yehova+ uli pa ine, chifukwa iye anandidzoza kuti ndilengeze uthenga wabwino kwa osauka. Anandituma kudzalalikira za kumasulidwa kwa ogwidwa ukapolo, ndi zoti akhungu ayambe kuona. Anandituma kudzamasula oponderezedwa kuti akhale mfulu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena