Yesaya 42:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Bango lophwanyika sadzalithyola,+ ndipo chingwe cha nyale chomwe chatsala pang’ono kuzima sadzachizimitsa. Iyeyo adzabweretsa chilungamo mokhulupirika.+ Mateyu 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Bango lophwanyika sadzalisansantha ndipo nyale yofuka sadzaizimitsa,+ kufikira atakwanitsa kubweretsa chilungamo.+
3 Bango lophwanyika sadzalithyola,+ ndipo chingwe cha nyale chomwe chatsala pang’ono kuzima sadzachizimitsa. Iyeyo adzabweretsa chilungamo mokhulupirika.+
20 Bango lophwanyika sadzalisansantha ndipo nyale yofuka sadzaizimitsa,+ kufikira atakwanitsa kubweretsa chilungamo.+