Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 72:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Aweruzire anthu milandu mwachilungamo,+

      Ndipo aweruze milandu ya osautsika ndi ziweruzo zolungama.+

  • Yesaya 11:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye adzasangalala ndi kuopa Yehova.+

      Sadzaweruza potengera zimene wangoona ndi maso ake, kapena kudzudzula potengera zimene wangomva ndi makutu ake.+

  • Mateyu 12:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Bango lophwanyika sadzalisansantha ndipo nyale yofuka sadzaizimitsa,+ kufikira atakwanitsa kubweretsa chilungamo.+

  • Yohane 5:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ine sindingachite chilichonse chongoganiza ndekha. Ndimaweruza malinga ndi mmene ndamvera, ndipo chiweruzo chimene ndimapereka n’cholungama,+ chifukwa sinditsatira chifuniro changa, koma chifuniro+ cha amene anandituma.

  • Chivumbulutso 19:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndipo nditayang’ana ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Wokwerapo wake dzina lake linali Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iyeyo anali kuweruza ndi kumenya nkhondo mwachilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena