Mateyu 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho atapita patsogolo pang’ono, anagwada mpaka nkhope yake pansi, ndipo anapemphera+ kuti: “Atate wanga, ngati n’kotheka, kapu+ iyi indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga,+ koma mwa kufuna kwanu.”+ Yohane 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anati: “Chakudya+ changa ndicho kuchita chifuniro+ cha amene anandituma ndi kutsiriza ntchito yake.+ Yohane 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Chifukwa ndinatsika kuchokera kumwamba+ kudzachita chifuniro cha iye amene anandituma, osati chifuniro changa.+
39 Choncho atapita patsogolo pang’ono, anagwada mpaka nkhope yake pansi, ndipo anapemphera+ kuti: “Atate wanga, ngati n’kotheka, kapu+ iyi indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga,+ koma mwa kufuna kwanu.”+
34 Yesu anati: “Chakudya+ changa ndicho kuchita chifuniro+ cha amene anandituma ndi kutsiriza ntchito yake.+
38 Chifukwa ndinatsika kuchokera kumwamba+ kudzachita chifuniro cha iye amene anandituma, osati chifuniro changa.+