Yohane 5:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma ine ndili ndi umboni woposa wa Yohane, pakuti ntchito zenizenizo zimene Atate wanga anandipatsa kuti ndizikwaniritse, ntchito zimene ine ndikuchita,+ zikundichitira umboni kuti Atate ananditumadi. Yohane 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndakulemekezani+ padziko lapansi, popeza ndatsiriza kugwira ntchito imene munandipatsa.+ Yohane 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atalandira vinyo wowawasayo, Yesu anati: “Ndakwaniritsa chifuniro chanu!”+ ndipo anaweramitsa mutu, ndi kupereka mzimu wake.+
36 Koma ine ndili ndi umboni woposa wa Yohane, pakuti ntchito zenizenizo zimene Atate wanga anandipatsa kuti ndizikwaniritse, ntchito zimene ine ndikuchita,+ zikundichitira umboni kuti Atate ananditumadi.
30 Atalandira vinyo wowawasayo, Yesu anati: “Ndakwaniritsa chifuniro chanu!”+ ndipo anaweramitsa mutu, ndi kupereka mzimu wake.+