Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 11:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Akhungu akuonanso,+ olumala+ akuyendayenda, akhate+ akuyeretsedwa ndipo ogontha+ akumva. Akufa+ akuukitsidwa, ndipo kwa aumphawi uthenga wabwino ukulengezedwa.+

  • Yohane 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iyeyu anabwera kwa Yesu usiku+ ndi kumuuza kuti: “Rabi,+ tikudziwa kuti inu ndinu mphunzitsi+ wochokera kwa Mulungu,+ chifukwa munthu sangathe kuchita zizindikiro+ zimene inu mumachita ngati Mulungu sali naye.”+

  • Yohane 7:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Komabe ochuluka m’khamu la anthulo anakhulupirira mwa iye+ ndipo anayamba kunena kuti: “Akadzafika Khristu, kodi adzachita zizindikiro zochuluka+ kuposa zimene munthu uyu wachita?”

  • Yohane 10:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Yesu anawayankha kuti: “Ndakuuzani kale, koma inu simukukhulupirira. Ntchito zimene ine ndikuchita m’dzina la Atate wanga, zikundichitira umboni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena