Maliko 5:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndiyeno anagwira dzanja la mwanayo ndi kunena kuti: “Talʹi·tha cuʹmi,” mawu amene powamasulira amatanthauza kuti: “Kamtsikana iwe, ndikunena ndi iwe, Dzuka!”+
41 Ndiyeno anagwira dzanja la mwanayo ndi kunena kuti: “Talʹi·tha cuʹmi,” mawu amene powamasulira amatanthauza kuti: “Kamtsikana iwe, ndikunena ndi iwe, Dzuka!”+