Mateyu 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atatulutsa anthu aja panja, iye analowa ndi kugwira dzanja la mtsikanayo,+ ndipo iye anadzuka.+ Luka 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atatero anayandikira ndi kugwira chithathacho. Pamenepo onyamulawo anangoima chilili, ndipo iye anati: “Mnyamata iwe, ndikunena ndi iwe, Dzuka!”+ Luka 8:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Koma iye anamugwira dzanja ndi kuitana kuti: “Mtsikana iwe, dzuka!”+ Machitidwe 9:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma Petulo anatulutsa anthu onse,+ ndiyeno anagwada pansi ndi kupemphera. Kenako anatembenukira mtembowo ndi kunena kuti: “Tabita, dzuka!” Pamenepo mayiyo anatsegula maso ake, ndipo mmene anaona Petulo, anadzuka n’kukhala tsonga.+
14 Atatero anayandikira ndi kugwira chithathacho. Pamenepo onyamulawo anangoima chilili, ndipo iye anati: “Mnyamata iwe, ndikunena ndi iwe, Dzuka!”+
40 Koma Petulo anatulutsa anthu onse,+ ndiyeno anagwada pansi ndi kupemphera. Kenako anatembenukira mtembowo ndi kunena kuti: “Tabita, dzuka!” Pamenepo mayiyo anatsegula maso ake, ndipo mmene anaona Petulo, anadzuka n’kukhala tsonga.+