Maliko 5:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kum’seka monyodola. Koma atawatulutsa onsewo, anatenga bambo ndi mayi a mwanayo ndi amene anali naye aja, ndipo analowa kumene kunali mwanayo.+ Luka 8:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Atafika kunyumbako sanalole kuti aliyense alowe naye kupatulapo Petulo, Yohane ndi Yakobo, komanso bambo ndi mayi a mtsikanayo.+
40 Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kum’seka monyodola. Koma atawatulutsa onsewo, anatenga bambo ndi mayi a mwanayo ndi amene anali naye aja, ndipo analowa kumene kunali mwanayo.+
51 Atafika kunyumbako sanalole kuti aliyense alowe naye kupatulapo Petulo, Yohane ndi Yakobo, komanso bambo ndi mayi a mtsikanayo.+