Mateyu 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yesu anawauza kuti: “Tulukani muno, pakuti mtsikanayu sanamwalire ayi, koma akugona.”+ Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kum’seka monyodola.+ Luka 8:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Atafika kunyumbako sanalole kuti aliyense alowe naye kupatulapo Petulo, Yohane ndi Yakobo, komanso bambo ndi mayi a mtsikanayo.+ Luka 8:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kumuseka monyodola, chifukwa anali kudziwa kuti wamwalira.+
24 Yesu anawauza kuti: “Tulukani muno, pakuti mtsikanayu sanamwalire ayi, koma akugona.”+ Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kum’seka monyodola.+
51 Atafika kunyumbako sanalole kuti aliyense alowe naye kupatulapo Petulo, Yohane ndi Yakobo, komanso bambo ndi mayi a mtsikanayo.+