Machitidwe 9:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Petulo anauza anthu onse kuti atuluke,+ ndiyeno anagwada nʼkupemphera. Kenako anatembenuka nʼkuyangʼana mtembowo nʼkunena kuti: “Tabita, dzuka!” Ndiyeno mayiyo anatsegula maso ndipo ataona Petulo, anadzuka nʼkukhala tsonga.+
40 Petulo anauza anthu onse kuti atuluke,+ ndiyeno anagwada nʼkupemphera. Kenako anatembenuka nʼkuyangʼana mtembowo nʼkunena kuti: “Tabita, dzuka!” Ndiyeno mayiyo anatsegula maso ndipo ataona Petulo, anadzuka nʼkukhala tsonga.+