Mateyu 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atatulutsa anthu aja panja, iye analowa ndi kugwira dzanja la mtsikanayo,+ ndipo iye anadzuka.+ Luka 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo wakufayo anadzuka ndi kukhala tsonga, ndipo anayamba kulankhula. Kenako anam’pereka kwa mayi ake.+ Yohane 11:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Atanena zimenezi, anafuula mokweza mawu kuti: “Lazaro, tuluka!”+
15 Pamenepo wakufayo anadzuka ndi kukhala tsonga, ndipo anayamba kulankhula. Kenako anam’pereka kwa mayi ake.+