1 Mafumu 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano Eliya anatenga mwanayo n’kutsika naye kuchokera kuchipinda chapadenga chija, n’kumupereka kwa mayi ake. Ndiyeno anati: “Taona, mwana wako ali moyo.”+ 2 Mafumu 4:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno Elisa anaitana Gehazi n’kumuuza kuti: “Itana mayi wachisunemu uja.”+ Gehazi anaitana mayiyo ndipo anabweradi kwa Elisa. Elisayo anauza mayiyo kuti: “Nyamulani mwana wanu.”+
23 Tsopano Eliya anatenga mwanayo n’kutsika naye kuchokera kuchipinda chapadenga chija, n’kumupereka kwa mayi ake. Ndiyeno anati: “Taona, mwana wako ali moyo.”+
36 Ndiyeno Elisa anaitana Gehazi n’kumuuza kuti: “Itana mayi wachisunemu uja.”+ Gehazi anaitana mayiyo ndipo anabweradi kwa Elisa. Elisayo anauza mayiyo kuti: “Nyamulani mwana wanu.”+