Luka 8:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Pamenepo mzimu wake+ unabwerera, ndipo nthawi yomweyo anadzuka.+ Ndiyeno anawauza kuti am’patse chakudya mtsikanayo.+
55 Pamenepo mzimu wake+ unabwerera, ndipo nthawi yomweyo anadzuka.+ Ndiyeno anawauza kuti am’patse chakudya mtsikanayo.+