Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+

  • Genesis 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Koma ine ndidzabweretsa chigumula+ chamadzi padziko lapansi, kuti chiwononge chamoyo+ chilichonse cha pansi pa thambo, chimene chili ndi mphamvu ya moyo* m’thupi mwake. Chilichonse cha m’dziko lapansi chidzafa.+

  • Yobu 33:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mzimu wa Mulungu unandiumba,+

      Mpweya wa Wamphamvuyonse unandipatsa moyo.+

  • Mlaliki 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pakuti ana a anthu ali ndi mapeto, ndipo zinyamanso zili ndi mapeto. Mapeto a zonsezi ndi ofanana.+ Nyama imafa ndipo munthunso amafa.+ Mzimu wa zonsezi ndi umodzi,+ moti munthu saposa nyama, pakuti zonse n’zachabechabe.

  • Yesaya 42:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mulungu woona Yehova, amene analenga kumwamba+ ndiponso Wokutambasula Wamkulu,+ amene anakhazikitsa dziko lapansi+ ndi zonse zimene zili mmenemo,+ amene anapereka mpweya+ kwa anthu amene ali mmenemo,+ ndi mzimu kwa anthu amene amayenda padzikopo,+ iye wanena kuti:

  • Chivumbulutso 11:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Masiku atatu ndi hafu+ aja atatha, mzimu wa moyo wochokera kwa Mulungu unalowa mwa mboni zija.+ Ndiyeno mbonizo zinaimirira, ndipo amene anali kuziona anagwidwa ndi mantha aakulu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena